You're welcome to MalawianCameras
YouTube Channel Here we do these things
Reactions
News updates and commentary
Fun videos
Vlogging
So feel free to interact with with us
We need your wisdom and support
Let's build the world together with love and respect and peace
Malawian Cameras
KUTSATSA MALONDA
Kwaomwe akufuna kuphunzira ma Phunziro a Computer Mwai ujatu uwu Ku Salima pa Takumana
1 month ago | [YT] | 30
View 3 replies
Malawian Cameras
Happy birthday To Mr Future President of Malawi
Denis Thanthwe Khang'a Mahata
2 months ago | [YT] | 225
View 47 replies
Malawian Cameras
๐๐๐๐๐
Brian Banda aaaaaaa Rest In Peace
Apa sizinayende What a big loss๐ฅน๐ฅน๐ฅน
2 months ago | [YT] | 262
View 55 replies
Malawian Cameras
#PlaneCrashProbe
Zomba City South: Nkhani ya chitetezo komanso nkhani yonena kuti ndege ikagwa sumufuna kuitana adani maka ndege ikakhala kuti yagwa, ichi ndi chifukwa chake ELT ya ndege yomwe tikukambilanayi inaikidwa pa off position?
Colonel Alex Mwachande: A serviceable ELT is always put at arm so this one was off because it wasn't working.
Zomba City South: Ndiye ngati siyimagwira ntchito chinali chifukwa choichosa pa arm ndikuika pa off?
Colonel Aex Mwachande: The ELT was not serviceable so putting it on the air would mean not being honest with what is on craft. But in this case it's the choice of whoever is making the checks they can either put it on the arm or off. And if it they put it on off the main reason is because it was off.
Zomba City South: Kusonyeza kuti ELT inaikidwa ku off cha ma 2006 umo?
Colonel Aex Mwachande: Eya
Zomba City South: Funsoli ndinafunsaso General omwe anbwera dzulo, kodi ndegeyi inagulidwa kuti ikhale ya VVIP ndiye inachita kusinthidwa kuti ikhale ya military?
Colonel Alex Mwachande: Eya inali ya VVIP
Zomba City South: Ndiye ngati inagulidwa ngati ya VVIP timadziwa kuti izakhala ndege ya civilian? Ndiye ndi chifukwa chani inalibe black box?
When the aircraft was being bought the manufacturer and the seller prescribed flight data recorder, cock pit recorder as optional. Ndipo pomwe ndegeyi inkabwera ku Malawi inalibe zinthuzi. Patatha zaka eni opanga ndegezi anaonjezela zinthu zina to improve design and efficiency. This was presented to us in form of a quotation as a mandatory in the European Union but not this part of Africa that it was being operated.
Wolemba Lydia Banda, Lilongwe
4 months ago | [YT] | 32
View 3 replies
Malawian Cameras
Welcome back!!
Tikhala ndi Thanthwe Khang'a Denis Mahata 8pm Sharp Lero Pa 10 June 2026 Kuli zinthutu Uku tikhale pomwepo......
Malawian Cameras
4 months ago (edited) | [YT] | 225
View 25 replies
Malawian Cameras
Donald Trump
Watumiza uthenga uwu moti apapa akuti ali kaye mu Situation Room akukapanga chiganizo chomaliza uthenga umene iye walemba ndi uwu๐๐๐๐๐๐๐๐
โIran iyenera kuvomera kuti sidzakhala konse ndi Chida cha Nyukiliya kapena Bomba. Strait ya Hormuz iyenera kutsegulidwa nthawi yomweyo, popanda misonkho iliyonse, kuti zombo ziziyenda momasuka mbali zonse ziwiri. Mabomba onse amโmadzi (water mines), ngati alipo, adzachotsedwa (ife tachotsa ambiri mwa kuwaphulitsa pogwiritsa ntchito makina athu amphamvu ochotsa mabomba amโmadzi. Iran idzamaliza kuchotsa kapena kuphulitsa mabomba onse otsala nthawi yomweyo, ndipo sadzakhala ambiri!). Zombo zomwe zinamangidwa mu Strait chifukwa cha kutsekedwa kwakukulu kwa nyanja ndi asilikali athu a panyanja, komwe tsopano kuchotsedwa, zitha kuyamba โkubwerera kwawo!โ Perekani moni kwa akazi anu, amuna anu, makolo anu, ndi mabanja anu kuchokera kwa ine, Purezidenti wanu wokondedwa! Zinthu zokhudzana ndi uranium yomwe yakwezedwa mphamvu, yomwe nthawi zina imatchedwa โNuclear Dust,โ yomwe ili yobisika kwambiri pansi pa nthaka ndi mapiri omwe pafupifupi adagwa chifukwa cha kuukira kwa ndege ya B2 Bomber miyezi 11 yapitayo, idzafukulidwa ndi United States (yomwe, monga tavomerezera, ndi dziko lokhalo limodzi ndi China lomwe lili ndi luso la makina ochitira zimenezi!), mogwirizana ndi Islamic Republic of Iran komanso International Atomic Energy Agency, ndipo ZIDZAWONONGEDWA. Sipadzakhala ndalama zomwe zidzaperekedwe mpaka titadziwitsanso. Zinthu zina, zosafunika kwambiri, zavomerezedwanso. Tsopano ndipita ku Situation Room kuti ndikapange chisankho chomaliza. Zikomo chifukwa cha chidwi chanu pa nkhaniyi!โ
5 months ago | [YT] | 70
View 14 replies
Malawian Cameras
Jomo wangopepesa basi kuti zithe๐.
Mfumu ya mzinda wa Blantyre Isaac Jomo Osman wabwera poyera ndikuvomereza zomwe zili mkanema wina yemwe akuonetsa iye akupanda khofi mai wina.
Izi zikutsatira kusamvana komwe kunabuka pakati pa Osman ndi mai-yu yemwe amam'ganizira kuti amagula katundu obedwa.
Zitachitika izi, boma komanso mabungwe ndi nthambi zina zinabwera poyera ndikudzudzula mchitidweu.
Koma kudzera mu kalata yake, Osman wati wavomereza kulakwa kwake kaamba koti anachita zinthu zosemphana ndi udindo wake.
"Ndikufuna ndinene kuti zomwe ndinachita sizoyenera..." Yatero kalatayo.
Malingana ndi kalatayo, ndi udindo wa mfumu ya mzinda kuwonetsetsa kuti anthu akukhala motetezeka, molemekezedwa komanso umoyo wabwino.
Pakadali pano, Osman wati, "ndine odzipereka pa kafukufuku aliyense pa nkhaniyi komanso kupepesa kwa 'mama'".
5 months ago | [YT] | 148
View 45 replies
Malawian Cameras
#Times360Malawi
Yemwe anali nduna ya za Chuma a Simplex Chithyola Banda amangidwa ndi apolisi (Fiscal) lero.
Malinga ndi lawyer wa a Chithyola a Jivason Kadzipatike kumangidwa kutsatitira chikalata (Warrant of arrest)chomwe chinatengedwa ku bwalo la Mkukula.
Pakali pano apolisi sananene chomwe awamangira. A Chithyola akadzipereka okha ku polisi.
By Mercy Matonga
6 months ago | [YT] | 96
View 12 replies
Malawian Cameras
Moni ndine Jackie walemba izi
Iran yasiya dziko liri kukamwa kakasu.
Chikhalire, zimadziwika kuti ali ndi ma misayilo ofika 2500km.
Nde mayiko ena amadalira ma base omwe ali kutali poti ma misayilowa sangafikeko.
Koma ma misayilo awili anaponyedwa ulendo wa 4000km. Kupita ku base ina ya amelika ku Diyego Garcia.
Anthuwa akusunga ma joker anji
7 months ago | [YT] | 228
View 29 replies
Malawian Cameras
Dzulo tinati mphekesera zosezi zitha Netanyahu akabwera live ndipo 1 hour ago wabwera live
Kusonyeza kuti alimoyo Gulukunyinda khakhakha ameneyu
Ubwino wake ife takhala tikukana kuti tinene nkhani yoti tilibe nayo umboni n'chifukwa sitinanene nao zoti wafa
Zikomo
7 months ago | [YT] | 127
View 80 replies
Load more